Daniel 1:13 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mupenye maonekedwe athu ndi maonekedwe a anyamata akudya chakudya cha mfumu; ndi monga umo muonera, muchitire anyamata anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mudzafananize maonekedwe athu ndi a anyamata amene akudya chakudya cha mfumu, ndi kuti mudzachite ndi anyamata anu monga momwe mudzawaonere.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mupenye maonekedwe athu ndi maonekedwe a anyamata akudya cakudya ca mfumu; ndi monga umo muonera, mucitire anyamata anu.