Daniel 1:16 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo kapitaoyo anachotsa chakudya chao ndi vinyo akadamwa, nawapatsa zomera m'nthaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho kapitawo anawachotsera chakudya ndi vinyo za ku nyumba yaufumu zija nawapatsa ndiwo zamasamba basi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo kapitaoyo anacotsa cakudya cao ndi vinyo akadamwa, nawapatsa zomera m'nthaka.