Daniel 1:6 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa awa tsono munali a ana a Yuda, Daniele, Hananiya, Misaele, ndi Azariya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakati pa amenewa panali ena ochokera ku Yuda: Danieli, Hananiya, Misaeli ndi Azariya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa awa tsono munali a ana a Yuda, Danieli, Hananiya, Misayeli, ndi Azariya.