Daniel 10:14 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndadzera tsono kukuzindikiritsa chodzagwera anthu a mtundu wako masiku otsiriza; pakuti masomphenyawo ndiwo a masiku a m'tsogolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano ndafika kuti ndidzakufotokozere zimene zidzachitika kwa anthu a mtundu wako kutsogolo. Ndipo pali masomphenya enanso okhudza nthawi imene ikudza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndadzera tsono kukuzindikiritsa codzagwera anthu a mtundu wako masiku otsiriza; pakuti masomphenyawo ndiwo a masiku a m'tsogolo.