Daniel 10:15 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atanena ndi ine monga mwa mau awa, ndinaweramitsa nkhope yanga pansi ndi kukhala duu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi yomwe ankanena izi kwa ine, ndinazolika nkhope yanga pansi kusowa chonena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo atanena ndi ine monga mwa mau awa, ndinaweramitsa nkhope yanga pansi ndi kukhala du.