Daniel 10:18 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anandikhudzanso wina, maonekedwe ake ngati munthu, nandilimbikitsa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka wooneka ngati munthu uja anandikhudzanso ndipo anandipatsa mphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anandikhudzanso wina, maonekedwe ace ngati munthu, nandilimbikitsa ine.