Daniel 10:2 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku aja ine Daniele ndinali kulira masabata atatu amphumphu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi imeneyi, ine Danieli ndinalira kwa masabata atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku aja ine Danieli ndinali kulira masabata atatu amphumphu,