Daniel 10:21 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndidzakufotokozera cholembedwa pa lemba la choonadi; ndipo palibe wina wakudzilimbikitsa pamodzi ndi ine, kutsutsana ndi aja, koma Mikaele kalonga wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ndikuwuza zimene zalembedwa mʼbuku la zoona koma palibe wondithandiza kulimbana nawo kupatula Mikayeli, kalonga wako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndidzakufotokozera colembedwa pa lemba la coonadi; ndipo palibe wina wakudzilimbikitsa pamodzi ndi ine, kutsutsana ndi aja, koma Mikaeli kalonga wanu.