Daniel 10:5 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndinakweza maso anga, ndinapenya ndi kuona munthu wovala bafuta, womanga m'chuuno ndi golide woona wa ku Ufazi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndinakweza maso ndipo ndinaona kuti pafupi ndi ine panali munthu wochokera ku Ufazi atavala zovala zosalala ndi lamba wa golide woyengeka bwino mʼchiwuno mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndinakweza maso anga, ndinapenya ndi kuona munthu wobvala bafuta, womanga m'cuuno ndi golidi woona wa ku Ufazi;