Daniel 10:8 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo ndinatsala ndekha, ndipo ndinaona masomphenya akuluwa, koma wosakhala ndi mphamvu ine; pakuti kukoma kwanga kunasandulika chivundi mwa ine, wosakhalanso ndi chimphamvu ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndinatsala ndekha, ndikuonetsetsa masomphenya a ulemererowa. Ndiye nkhope yanga inasinthika, ndinalefuka, ndipo ndinalibenso mphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo ndinatsala ndekha, ndipo ndinaona masomphenya akuruwa, koma wosakhala ndi mphamvu ine; pakuti kukoma kwanga kunasandulika cibvundi mwa ine, wosakhalanso ndi mphamvu ine.