Daniel 10:9 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinamva kunena kwa mau ake, ndipo pamene ndinamva kunena kwa mau ake ndinagwidwa ndi tulo tatikulu pankhope panga, nkhope yanga pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka ndinamva iye akuyankhula, ndipo pamene ndinkamvetsera, ndinagwa chafufumimba ndi kugona tulo tofa nato.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinamva kunena kwa mau ace, ndipo pamene ndinamva kunena kwa mau ace ndinagwidwa ndi tulo tatikuru pankhope panga, nkhope yanga pansi.