Daniel 11:12 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atauchotsa unyinjiwo udzakwezeka mtima wake; ndipo adzagwetsa zikwi makumimakumi, koma sadzalakika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu la nkhondoli likadzagwidwa, mfumu yakummwera idzayamba kudzikuza ndipo idzapha anthu miyandamiyanda, koma kupambanaku sikudzapitirira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ataucotsa unyinjiwo udzakwezeka mtima wace; ndipo adzagwetsa zikwi makumi makumi, koma sadzalakika.