Daniel 11:26 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde iwo akudyako chakudya chake adzamuononga; ndi ankhondo ake adzasefukira, nadzagwa ambiri ophedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene amadya chakudya ndi mfumu adzamuukira; gulu lake lankhondo lidzagonjetsedwa, ndipo ambiri adzafera ku nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde iwo akudyako cakudya cace adzamuononga; ndi ankhondo ace adzasefukira, nadzagwaambiri ophedwa.