Daniel 11:29 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa nthawi yoikika adzabwera, nadzalowa kumwera; koma sikudzakhala monga nthawi yoyamba ija, kapena yotsirizayi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Patapita nthawi mfumu ya kumpoto idzabwereranso kummwera koma sidzapambana monga inachitira kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa nthawi yoikika adzabwera, nadzalowa kumwela; koma sikudzakhala monga nthawi yoyamba ija, kapena yotsirizayi.