Daniel 11:3 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo idzauka mfumu yamphamvu, nidzachita ufumu ndi ulamuliro waukulu, nidzachita monga mwa chifuniro chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mfumu yamphamvu idzafika imene idzalamulira ndi ufumu waukulu ndi kuchita zimene ifuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo idzauka mfumu yamphamvu, nidzacita ufumu ndi ulamuliro waukuru, nidzacita monga mwa cifuniro cace.