Daniel 11:41 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzalowanso m'dziko lokometsetsalo ndi maiko ambiri adzapasuka; koma opulumuka dzanja lake ndi awa: Edomu, ndi Mowabu, ndi oyamba a ana a Amoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Idzalowanso mʼDziko Lokongola ndipo anthu ambiri adzaphedwa. Koma Edomu, Mowabu ndi olamulira a Amoni adzapulumuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzalowanso m'dziko lokometsetsalo ndi maiko ambiri adzapasuka; koma opulumuka dzanja lace ndi awa: Edomu, ndi Moabu, ndi oyamba a ana a Amoni.