Daniel 11:43 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzachita mwamphamvu ndi chuma cha golide, ndi siliva, ndi zinthu zofunika zonse za Ejipito; Libiya ndi Akusi adzatsata mapazi ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Idzalanda chuma cha golide, siliva, ndi zonse za mtengowapatali za ku Igupto, ndiponso anthu a ku Libiya ndi Akusi adzagonja kwa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzacita mwamphamvu ndi cuma ca golidi, ndi siliva, ndi zinthu zofunika zonse za Aigupto; Alubi ndi Akusi adzatsata mapazi ace.