Daniel 11:44 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mbiri yochokera kum'mawa ndi kumpoto idzamvuta; nadzatuluka iye ndi ukali waukulu kupha ndi kuononga konse ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma uthenga wochokera kummawa ndi kumpoto udzayiopsa, ndipo idzapita ndi ukali kukawononga ndi kutheratu anthu ambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mbiri yocokera kum'mawa ndi kumpoto idzambvuta; nadzaturuka iye ndi ukali waukuru kupha ndi kuononga konse ambiri.