Daniel 11:5 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mfumu ya kumwera, ndiye wina wa akalonga ake, idzamposa mphamvu, nidzakhala nao ulamuliro; ulamuliro wake ndi ulamuliro waukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mfumu ya kummwera idzakhala yamphamvu, koma mmodzi mwa akalonga ake adzakhala ndi mphamvu kuposa iyo; adzalamulira ufumu wake waukulu kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mfumu ya kumwela, ndiye wina wa akalonga ace, idzamposa mphamvu, nidzakhala nao ulamuliro; ulamuliro wace ndi ulamuliro waukuru.