Daniel 11:9 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzalowa m'ufumu wa mfumu ya kumwera, koma adzabwera m'dziko lakelake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka mfumu ya kumpoto idzathira nkhondo dziko la mfumu ya kummwera koma idzalephera ndi kubwerera kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzalowa m'ufumu wa mfumu ya kumwela, koma adzabwera m'dziko lace lace.