Daniel 12:13 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwe, muka mpaka chimaliziro; pakuti udzapumula, nudzaima m'gawo lako masiku otsiriza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma iweyo Danieli, pitiriza ndipo ulimbikire mpaka matsiriziro. Kenaka udzamwalira. Koma mʼmasiku otsiriza udzauka kuti ulandire gawo lako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwe, muka mpaka cimariziro; pakuti udzapumula, nudzaima m'gawo lako masiku otsiriza.