Daniel 12:2 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ambiri a iwo ogona m'fumbi lapansi adzauka, ena kunka kumoyo wosatha, ndi ena kumanyazi ndi mnyozo wosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambiri mwa amene akugona mʼnthaka adzadzuka: ena adzapita ku moyo wosatha, ena ku malo amanyazi ndi chilango chosatha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ambiri, a iwo ogona m'pfumbi lapansi adzauka, ena kumka ku moyo wosatha, ndi ena ku manyazi ndi mnyozo wosatha.