Daniel 12:8 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinachimva ichi, koma osachizindikira; pamenepo ndinati Mbuye wanga, chitsiriziro cha izi nchiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinamva, koma sindinamvetsetse. Choncho ndinafunsa kuti, “Mbuye wanga, nanga matsiriziro a zonsezi adzakhala chiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinacimva ici, koma osacizindikira; pamenepo ndinati Mbuye wanga, citsiriziro ca izi nciani?