Daniel 12:9 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati, Pita Daniele; pakuti mauwo atsekedwa, nakomeredwa chizindikiro mpaka nthawi ya chitsiriziro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anandiyankha kuti, “Pita iwe Danieli, pakuti mawuwa ndi osungidwa ndi omatidwa kufikira nthawi ya chimaliziro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati, Pita Danieli; pakuti mauwo atsekedwa, nakomeredwa cizindikilo mpaka nthawi ya citsiriziro.