Daniel 2:12 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake mfumu inakwiya, nizaza kwambiri, nilamulira kuti awaphe anzeru onse m'Babiloni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimenezi zinapsetsa mtima mfumu ndipo inakwiya kwambiri kotero inalamula kuti anzeru onse a ku Babuloni aphedwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace mfumu inakwiya, nizaza kwambiri, nilamulira kuti awaphe anzeru onse m'Babulo.