Daniel 2:13 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mwemo chilamulirocho chidamveka, ndi eni nzeru adati aphedwe; anafunafunanso Daniele ndi anzake aphedwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho lamulo linaperekedwa kuti anthu anzeru aphedwe, ndipo anatuma anthu kukafunafuna Danieli ndi anzake kuti iwonso aphedwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mwemo cilamuliroco cidamveka, ndi eni nzeru adati aphedwe; anafuna-funanso Danieli ndi anzace aphedwe.