Daniel 2:22 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye avumbulutsa zinthu zakuya ndi zinsinsi; adziwa zokhala mumdima, ndi kuunika kumakhala kwa Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amavumbulutsa zinthu zozama ndi zobisika; amadziwa zimene zili mu mdima, ndipo kuwunika kumakhala ndi Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye abvumbulutsa zinthu zakuya ndi zinsinsi; adziwa zokhala mumdima, ndi kuunika kumakhala kwa Iye.