Daniel 2:26 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu inayankha, niti kwa Daniele, amene dzina lake ndiye Belitesazara, Ukhoza kodi kundidziwitsa lotolo ndidalilota, ndi kumasulira kwake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inafunsa Danieli (wotchedwanso Belitesezara) kuti, “Kodi ukhoza kundiwuza zomwe ine ndinaona mʼmaloto anga ndi tanthauzo lake?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu inayankha, niti kwa Danieli, amene dzina lace ndiye Belitsazara, Ukhoza kodi kundidziwitsa lotolo ndidalilota, ndi kumasulira kwace?