Daniel 2:27 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nayankha Daniele pamaso pa mfumu, nati, Chinsinsi inachitira liuma mfumu, angakhale anzeru, openduza, alembi, kapena alauli, sakhoza kuchiululira mfumu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Danieli anayankha kuti, “Palibe munthu wanzeru, wowombeza, wamatsenga kapena wamawula amene akhoza kufotokozera mfumu chinsinsi chimene mwafuna kudziwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nayankha Danieli pamaso pa mfumu, nati, Cinsinsi inacitira liuma mfumu, angakhale anzeru, openduza, alembi, kapena alauli, sakhoza kuciululira mfumu;