Daniel 2:3 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Niti nao mfumu, Ndalota loto, nuvutika mzimu wanga kudziwa lotolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mfumuyo inawawuza kuti, “Ndalota loto lomwe likundisautsa ndipo ndikufuna kudziwa tanthauzo lake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Niti nao mfumu, Ndalota loto, nubvutika mzimu wanga kudziwa lotolo.