Daniel 2:32 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Fano ili tsono, mutu wake unali wagolide wabwino, chifuwa chake ndi manja ake zasiliva, mimba yake ndi chuuno chake zamkuwa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mutu wa chowumbacho unali wagolide wabwino kwambiri. Chifuwa ndi manja ake zinali zasiliva. Mimba ndi ntchafu zake zinali zamkuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pano ili tsono, mutu wace unali wagolidi wabwino, cifuwa cace ndi manja ace zasiliva, mimba yace ndi cuuno cace zamkuwa,