Daniel 2:34 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munali chipenyere kufikira mwala unasemedwa popanda manja, umene unagunda fanoli pa mapazi ake okhala chitsulo ndi dongo, nuwaphwanya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mukuona, mwala unagamuka, koma osati ndi manja a munthu. Unagwera fanolo pa mapazi ake achitsulo chosakaniza ndi dongo aja ndi kuwaphwanya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munali cipenyere kufikira mwala unasemedwa popanda manja, umene unagunda fanoli pa mapazi ace okhala citsulo ndi dongo, nuwaphwanya.