Daniel 2:37 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu mfumu ndinu mfumu ya mafumu, pakuti Mulungu wa Kumwamba anakupatsani ufumu, ndi mphamvu yaikulu, ndi ulemu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mfumu, ndinu mfumu ya mafumu. Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu, ulamuliro ndi mphamvu ndi ulemerero;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu mfumu ndinu mfumu ya mafumu, pakuti Mulungu wa Kumwamba anakupatsani ufumu, ndi mphamvu yaikuru, ndi ulemu;