Daniel 2:46 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo mfumu Nebukadinezara anagwa nkhope yake pansi, nalambira Daniele, nati amthirire nsembe yaufa ndi ya zonunkhira zokoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo mfumu Nebukadinezara inadzigwetsa chafufumimba pamaso pa Danieli ndi kumupatsa ulemu. Ndipo inalamula kuti anthu onse amuthirire Danieli nsembe ndi kumufukizira lubani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo mfumu Nebukadinezara anagwa nkhope yace pansi, nalambira Danieli, nati amthirire nsembe yaufa ndi ya zonunkhira zokoma.