Daniel 2:49 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Daniele anapempha mfumu, ndipo anaika Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego, ayang'anire ntchito za dera la ku Babiloni. Koma Daniele anakhala m'bwalo la mfumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso, monga mwa pempho la Danieli, mfumu inayika Sadirake, Mesaki ndi Abedenego, kuti akhale oyangʼanira chigawo cha Babuloni, pamene Danieliyo ankakhazikika mʼbwalo la mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Danieli anapempha mfumu, ndipo anaika Sadrake, Mesake, ndi Abedinego, ayang'anire nchito za dera la ku Babulo. Koma Danieli anakhala m'bwalo la mfumu.