Daniel 2:6 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mukandidziwitsa lotoli, ndi kumasulira kwake, mudzalandira kwa ine mphatso, ndi mphotho, ndi ulemu waukulu; chifukwa chake mundidziwitse lotoli ndi kumasulira kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati mundiwuza zimene ndalota ndi tanthauzo lake, ndidzakupatsani mphatso ndi mphotho ndi ulemu waukulu. Choncho mundiwuze zimene ndalota ndi tanthauzo lake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mukandidziwitsa lotoli, ndi kumasulira kwace, mudzalandira kwa ine mphatso, ndi mphotho, ndi ulemu waukuru; cifukwa cace mundidziwitse lotoli ndi kumasulira kwace.