Daniel 2:8 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu inayankha, niti, Ndidziwatu kuti mukunkhuniza dala, pakuona inu kuti chinthuchi chandichokera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mfumu inayankha kuti, “Ine ndikudziwa kuti mukungozengereza kufuna kutaya nthawi chabe chifukwa mukuzindikira kuti izi ndi zimene ndatsimikiza kuchita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu inayankha, niti, Ndidziwatu kuti mukunkhuniza dala, pakuona inu kuti cinthuci candicokera.