Daniel 3:11 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi yense wosagwadira ndi kulambira adzaponyedwa m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi kuti aliyense osalambira ndi kupembedza adzaponyedwa mʼngʼanjo ya moto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi yense wosagwadira ndi kulambiraadzaponyedwa m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto.