Daniel 3:18 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akapanda kutero, dziwani, mfumu, kuti sitidzatumikira milungu yanu, kapena kulambira fano lagolide mudaliimikalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngakhale Mulungu wathu atapanda kutipulumutsa, tikufuna mudziwe inu mfumu, kuti sitidzatumikira milungu yanu kapena kupembedza fano la golide limene munaliyimika.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akapanda kutero, dziwani, mfumu, kuti sitidzatumikira milungu yanu, kapena kulambira fano lagolidi mudaliimikalo.