Daniel 3:20 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nauza amuna ena amphamvu a m'khamu lake la nkhondo amange Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego, ndi kuwaponya m'ng'anjo yotentha yamoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo analamula ena mwa asilikali amphamvu kwambiri mʼgulu lake lankhondo kuti amange Sadirake, Mesaki ndi Abedenego ndi kuwaponya mʼngʼanjo ya moto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nauza amuna ena amphamvu a m'khamu lace la nkhondo amange Sadrake, Mesake, ndi Abedinego, ndi kuwaponya m'ng'anjo yotentha yamoto.