Daniel 3:22 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Motero, popeza mau a mfumu anafulumiza, ndi ng'anjo inatentha koposa, lawi la moto linapha iwo aja ananyamula Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono popeza lamulo la mfumu linali lofulumiza, ngʼanjo inatenthetsedwa kowirikiza mwakuti malawi ake anapha asilikali amene ananyamula Sadirake, Mesaki ndi Abedenego,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Motero, popeza mau a mfumu anafulumiza, ndi ng'anjo inatentha koposa, lawi la moto linapha iwo aja ananyamula Sadrake, Mesake, ndi Abedinego.