Daniel 3:23 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amuna atatu awa, Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego, anagwa pansi omangidwa m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anyamata atatuwa, ali chimangidwire, anagwera mʼngʼanjo ya moto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amuna atatu awa, Sadrake, Mesake, ndi Abedinego, anagwa pansi omangidwa m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto.