Daniel 3:4 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wolalikira anafuulitsa, kuti, Akulamulirani inu anthu, mitundu ya anthu a manenedwe osiyana,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Inu anthu a mitundu yonse ndi a ziyankhulo zonse, mukulamulidwa kuti muchite izi: mitundu ya anthu ndi a chiyankhulo chilichonse
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wolalikira anapfuulitsa, kuti, Akulamulirani inu anthu, mitundu ya anthu a manenedwe osiyana,