Daniel 3:8 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anayandikira Ababiloni ena nthawi yomweyi, naneneza Ayuda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi imeneyi alawuli ena anafika ndi kuwanenera zoyipa Ayuda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anayandikira Akasidi ena nthawi yomweyi, naneneza Ayuda.