Daniel 4:1 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu Nebukadinezara, kwa anthu mitundu ya anthu, ndi a manenedwe okhala pa dziko lonse lapansi: Mtendere uchulukire inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Nebukadinezara anatumiza mawu awa kwa anthu a mitundu yonse, ndi chiyankhulo chilichonse, amene amakhala pa dziko lonse lapansi: Mtendere uchuluke pakati panu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu Nebukadinezara, kwa anthu, mitundu ya anthu, ndi a manenedwe okhala pa dziko lonse lapansi: Mtendere ucurukire inu.