Daniel 4:10 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masomphenya a m'mtima mwanga pakama panga ndi awa: Ndinapenya ndi kuona mtengo pakati pa dziko lapansi, msinkhu wake ndi waukulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndi masomphenya amene ine ndinaona pamene ndinali kugona pa bedi: Ndinaona, mtengo wautali kwambiri utayima pakati pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masomphenya a m'mtima mwanga pakama panga ndi awa: Ndinapenya ndi kuona mtengo pakati pa dziko lapansi, msinkhu wace ndi waukuru.