Daniel 4:2 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chandikomera kuonetsa zizindikiro ndi zozizwa, zimene anandichitira Mulungu Wam'mwambamwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chandikomera kukuwuzani zizindikiro zozizwitsa ndi zodabwitsa zimene Mulungu Wammwambamwamba wandichitira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Candikomera kuonetsa zizindikilo ndi zozizwa, zimene anandicitira Mulungu Wam'mwambamwamba.