Daniel 4:20 — Compare Translations

3 translations compared side by side

Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtengo mudauona umene unakula, nukhala wolimba, nufikira kumwamba msinkhu wake, nuonekera pa dziko lonse lapansi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtengo munawuona uja, umene unkakulirakulira kwambiri ndi kulimba, ndi msonga yake inafika mlengalenga, ndi kuonekera ku dziko lonse lapansi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtengo mudauona umene unakula, nukhala wolimba, nufikira kumwamba msinkhu wace, nuonekera pa dziko lonse lapansi,