Daniel 4:24 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kumasulira kwake ndi uku, mfumu; ndipo chilamuliro cha Wam'mwambamwamba chadzera mbuye wanga mfumu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tanthauzo lake ndi ili mfumu, izi ndi zimene Mulungu Wammwambamwamba watsimikiza kuti zikugwereni mbuye wanga mfumu:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kumasulira kwace ndi uku, mfumu; ndipo cilamuliro ca Wam'mwambamwamba cadzera mbuye wanga mfumu: