Daniel 4:26 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kuti anauza asiye chitsa ndi mizu ya mtengo, ufumu wanu udzakhazikikira inu, mukakatha kudziwa kuti Kumwamba kumalamulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lamulo losiya tsinde la mtengo ndi mizu yake litanthauza kuti ufumu wanu udzabwezeredwa kwa inu mukadzavomereza kuti Mulungu ndiye amalamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kuti anauza asiye citsa ndi mizu ya mtengo, ufumu wanu udzakhazikikira inu, mukakatha kudziwa kuti Kumwamba kumalamulira.